Masalimo 47:2 - Buku Lopatulika2 Pakuti Yehova Wam'mwambamwamba ndiye woopsa; ndiye mfumu yaikulu padziko lonse lapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Pakuti Yehova Wam'mwambamwamba ndiye woopsa; ndiye mfumu yaikulu pa dziko lonse lapansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Paja Chauta Wopambanazonse, ndi woopsa, ndiye mfumu yaikulu pa dziko lonse lapansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ndi woopsadi Yehova Wammwambamwamba; Mfumu yayikulu ya dziko lonse lapansi! Onani mutuwo |