Masalimo 47:1 - Buku Lopatulika1 Ombani m'manja, mitundu yonse ya anthu; fuulirani kwa Mulungu ndi liu la kuimbitsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ombani m'manja, mitundu yonse ya anthu; fuulirani kwa Mulungu ndi liu la kuimbitsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Ombani m'manja inu anthu a mitundu yonse. Fuulani kwa Mulungu poimba nyimbo zachimwemwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Ombani mʼmanja, inu anthu onse; fuwulani kwa Mulungu ndi mawu achimwemwe. Onani mutuwo |