Masalimo 45:16 - Buku Lopatulika16 M'malo mwa makolo ako mudzakhala ana ako, udzawaika akhale mafumu m'dziko lonse lapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 M'malo mwa makolo ako mudzakhala ana ako, udzawaika akhale mafumu m'dziko lonse lapansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Inutu zidzukulu zanu zidzaloŵa m'malo mwa makolo anu, mudzaŵasandutsa mafumu pa dziko lonse lapansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ana ako aamuna adzatenga malo a makolo ako; udzachititsa kuti akhale ana a mfumu mʼdziko lonse. Onani mutuwo |