Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 3:1 - Buku Lopatulika

1 Yehova! Ha! Achuluka nanga akundisautsa ine! Akundiukira ine ndi ambiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Yehova! Ha! Achuluka nanga akundisautsa ine! Akundiukira ine ndi ambiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Inu Chauta, ndili ndi adani ochuluka, anthu ambiri akundiwukira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Inu Yehova, achulukadi adani anga! Achulukadi amene andiwukira!

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 3:1
7 Mawu Ofanana  

Ndipo Abisalomu, ndi anthu onse aamuna a Israele, anafika ku Yerusalemu, ndi Ahitofele pamodzi naye.


Onetsani chifundo chanu chodabwitsa, Inu wakupulumutsa okhulupirira Inu kwa iwo akuwaukira ndi dzanja lanu lamanja.


Ndipo mbale adzapereka mbale wake kuimfa, ndi atate mwana wake: ndipo ana adzatsutsa akuwabala, nadzawafetsa iwo.


Ndipo anthu onse anavomereza, ndi kuti, Mwazi wake uli pa ife ndi pa ana athu.


Ndipo mafumu awa onse anasonkhana, nadza namanga pamodzi ku madzi a Meromu, kumthira Israele nkhondo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa