Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 28:8 - Buku Lopatulika

8 Yehova ndiye mphamvu yao, inde mphamvu ya chipulumutso cha wodzozedwa wake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Yehova ndiye mphamvu yao, inde mphamvu ya chipulumutso cha wodzozedwa wake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Chauta ndiye mphamvu zimene anthu ake amadalira, ndiye kothaŵira komwe wodzozedwa wake amapulumukirako.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Yehova ndi mphamvu ya anthu ake, linga la chipulumutso kwa wodzozedwa wake.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 28:8
6 Mawu Ofanana  

Yehova Ambuye, ndinu mphamvu ya chipulumutso changa, munandiphimba mutu wanga tsiku lakulimbana nkhondo.


Adzikhazikitsa mafumu a dziko lapansi, nachita upo akulu pamodzi, Kutsutsana naye Yehova, ndi Wodzozedwa wake, ndi kuti,


Tsopano ndidziwa kuti Yehova apulumutsa wodzozedwa wake; adzamvomereza mu Mwamba mwake moyera ndi mphamvu ya chipulumutso cha dzanja lake lamanja.


Ena atama magaleta, ndi ena akavalo; koma ife tidzatchula dzina la Yehova Mulungu wathu.


Mzimu wa Ambuye Yehova uli pa ine; pakuti Yehova wandidzoza ine ndilalikire mau abwino kwa ofatsa; Iye wanditumiza ndikamange osweka mtima, ndikalalikire kwa am'nsinga mamasulidwe, ndi kwa omangidwa kutsegulidwa kwa m'ndende;


Pamenepo Samuele anatenga nyanga ya mafuta, namdzoza pakati pa abale ake; ndipo mzimu wa Yehova unalimbika pa Davide kuyambira tsiku lomweli. Ndipo Samuele ananyamuka, nanka ku Rama.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa