Masalimo 28:6 - Buku Lopatulika6 Wodalitsika Yehova, Pakuti adamva mau a kupemba kwanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Wodalitsika Yehova, Pakuti adamva mau a kupemba kwanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Chauta atamandike, pakuti wamva liwu la kupempha kwanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Matamando apite kwa Yehova, popeza Iye wamva kupempha chifundo kwanga. Onani mutuwo |