Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 26:2 - Buku Lopatulika

2 Mundiyesere, Yehova, ndipo mundisunthe; yeretsani impso zanga ndi mtima wanga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Mundiyesere, Yehova, ndipo mundisunthe; yeretsani impso zanga ndi mtima wanga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Mundiyang'anitsitse, Inu Chauta, ndi kundiyesa. Muwone mtima wanga pamodzi ndi maganizo anga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Patseni mayeso, Inu Yehova ndipo ndiyeseni, santhulani mtima wanga ndi maganizo anga;

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 26:2
8 Mawu Ofanana  

Mphulupulu zanga ndi zochimwa zanga ndi zingati? Mundidziwitse kulakwa kwanga ndi tchimo langa.


Mwayesera mtima wanga; mwandizonda usiku; mwandisuntha, simupeza kanthu; mwatsimikiza mtima kuti m'kamwa mwanga simudzalakwa.


Pakuti munatiyesera, Mulungu, munatiyenga monga ayenga siliva.


Ithe mphulupulu ya anthu oipa, ndikupemphani, koma wolungamayo mumkhazikitse. Pakuti woyesa mitima ndi impso ndiye Mulungu wolungama.


Koma, Inu Yehova wa makamu, amene muyesa olungama, amene muona impso ndi mtima, mundionetse ine kubwezera chilango kwanu pa iwo; pakuti kwa inu ndaululira mlandu wanga.


Ndi gawo lachitatulo ndidzalitengera kumoto, ndi kuwayenga ngati ayenga siliva, ndi kuwayesa monga ayesa golide; adzaitana dzina langa, ndipo ndidzawamvera; ndidzati, Awa ndi anthu anga; ndi iwo adzati, Yehova ndi Mulungu wanga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa