Masalimo 26:1 - Buku Lopatulika1 Mundiweruze, Yehova, pakuti ndayenda mu ungwiro wanga, ndipo ndakhulupirira Yehova, sindadzaterereka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Mundiweruze, Yehova, pakuti ndayenda m'ungwiro wanga, ndipo ndakhulupirira Yehova, sindadzaterereka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Inu Chauta, onetsani kuti ine ndine wosalakwa, pakuti ndimachita zolungama, ndipo ndakhulupirira Inu mosakayika konse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Weruzeni Inu Yehova pakuti ndakhala moyo wosalakwa. Ndadalira Yehova popanda kugwedezeka. Onani mutuwo |