Masalimo 25:22 - Buku Lopatulika22 Ombolani Israele, Mulungu, m'masautso ake onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ombolani Israele, Mulungu, m'masautso ake onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Inu Mulungu apulumutseni m'mavuto ao onse anthu anu Aisraele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Wombolani Israeli Inu Mulungu, ku mavuto ake onse! Onani mutuwo |