Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 24:8 - Buku Lopatulika

8 Mfumu imene ya ulemerero ndani? Yehova wamphamvu ndi wolimba, Yehova wolimba kunkhondo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Mfumu imene ya ulemerero ndani? Yehova wamphamvu ndi wolimba, Yehova wolimba kunkhondo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Kodi Mfumu yaulemereroyo ndani? Ndi Chauta wanyonga ndi wamphamvu, Chauta ndiye ngwazi pa nkhondo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Kodi Mfumu yaulemereroyo ndani? Yehova Wamphamvuzonse, Yehova ndiye wamphamvu pa nkhondo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 24:8
11 Mawu Ofanana  

Mulungu wa milungu, Yehova, wanena, aitana dziko lapansi kuyambira kutuluka kwa dzuwa kufikira kulowa kwake.


Yehova achita ufumu; wadziveka ndi ukulu; wadziveka Yehova, wadzimangirira mphamvu m'chuuno; dziko lomwe lokhalamo anthu likhakizika, silidzagwedezeka.


Yehova ndiye wankhondo; dzina lake ndiye Yehova.


Pakuti kwa ife mwana wakhanda wabadwa, kwa ife mwana wamwamuna wapatsidwa; ndipo ulamuliro udzakhala pa phewa lake, ndipo adzamutcha dzina lake Wodabwitsa, Wauphungu, Mulungu wamphamvu, Atate Wosatha, Kalonga wa mtendere.


atavula maukulu ndi maulamuliro, anawaonetsera poyera, nawagonjetsera nako.


Ndipo ndinapenya, ndipo taonani, kavalo woyera, ndipo womkwerayo anali nao uta; ndipo anampatsa korona; ndipo anatulukira wogonjetsa kuti akagonjetse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa