Masalimo 24:9 - Buku Lopatulika9 Weramutsani mitu yanu, zipata inu; inde weramutsani, zitseko zosatha inu, kuti Mfumu ya ulemerero ilowe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Weramutsani mitu yanu, zipata inu; inde weramutsani, zitseko zosatha inu, kuti Mfumu ya ulemerero ilowe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Kankhani zipata za mzinda, tsekulani zitseko zakalekalezo, kuti Mfumu yaulemerero iloŵe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Tukulani mitu yanu, inu zipata; tsekukani, inu zitseko zakalekalenu, kuti Mfumu yaulemerero ilowe. Onani mutuwo |