Masalimo 24:6 - Buku Lopatulika6 Uwu ndi mbadwo wa iwo akufuna Iye, iwo akufuna nkhope yanu, Mulungu wa Yakobo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Uwu ndi mbadwo wa iwo akufuna Iye, iwo akufuna nkhope yanu, Mulungu wa Yakobo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Anthu otere ndiwo amene amafunitsitsa Chauta, ndiwo amene amabwera kudzapembedza Mulungu wa Yakobe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Umenewo ndiwo mʼbado wa amene amafunafuna Yehova; amene amafunafuna nkhope yanu, Inu Mulungu wa Yakobo. Sela Onani mutuwo |