Masalimo 24:4 - Buku Lopatulika4 Woyera m'manja, ndi woona m'mtima, ndiye; iye amene sanakweze moyo wake kutsata zachabe, ndipo salumbira monyenga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Woyera m'manja, ndi woona m'mtima, ndiye; iye amene sanakweze moyo wake kutsata zachabe, ndipo salumbira monyenga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ndi amene amachita zabwino ndi manja ake, ndipo amaganiza zabwino mumtima mwake. Ndi amene salingalira zonama, ndipo salumbira monyenga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Iye amene ali ndi mʼmanja moyera ndi mtima woyera, amene sapereka moyo wake kwa fano kapena kulumbira mwachinyengo. Onani mutuwo |