Masalimo 24:3 - Buku Lopatulika3 Adzakwera ndani m'phiri la Yehova? Nadzaima m'malo ake oyera ndani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Adzakwera ndani m'phiri la Yehova? Nadzaima m'malo ake oyera ndani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ndani angayenere kukwera phiri la Chauta? Ndani angaime m'malo ake oyera? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ndani angakwere phiri la Yehova? Ndani angathe kuyima pa malo ake opatulika? Onani mutuwo |