Masalimo 24:2 - Buku Lopatulika2 Pakuti Iye analimanga pazinyanja, nalikhazika pamadzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Pakuti Iye analimanga pazinyanja, nalikhazika pamadzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Pakuti iye ndi amene adaika dziko lapansi pa nyanja yaikulu, adalikhazika pa mitsinje yozama. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 pakuti Iye ndiye anayika maziko ake pa nyanja ndi kulikhazika pamwamba pa madzi. Onani mutuwo |