Masalimo 21:8 - Buku Lopatulika8 Dzanja lanu lidzapeza adani anu onse, dzanja lanu lamanja lidzapeza iwo akuda Inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Dzanja lanu lidzapeza adani anu onse, dzanja lanu lamanja lidzapeza iwo akuda Inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Idzagonjetsa adani ake onse. Dzanja lake lamphamvu lidzakantha onse odana nayo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Dzanja lanu lidzayimitsa adani anu onse; dzanja lanu lamanja lidzagwira adani anu. Onani mutuwo |