Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 21:13 - Buku Lopatulika

13 Kwezekani, Yehova, mu mphamvu yanu; potero tidzaimba ndi kulemekeza chilimbiko chanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Kwezekani, Yehova, mu mphamvu yanu; potero tidzaimba ndi kulemekeza chilimbiko chanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Mutamandike, Inu Chauta, chifukwa cha kupambana kwanu. Tidzaimba ndi kuyamika mphamvu zanu zazikulu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Mukwezeke Inu Yehova mʼmphamvu yanu, ife tidzayimba nyimbo ndi kutamanda mphamvu yanu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 21:13
16 Mawu Ofanana  

Ukulu, ndi mphamvu, ndi ulemerero, ndi chipambano, ndi chifumu ndi zanu, Yehova; pakuti zonse zam'mwamba ndi padziko lapansi ndi zanu; ufumu ndi wanu, Yehova; ndipo mwakwezeka mutu wa pa zonse.


Tikanena za mphamvu, si ndiye wamphamvu? Tikanena za kuweruza, adzamuitana ndani?


Akunga Yehova Mulungu wathu ndani? Amene akhala pamwamba patali,


Yehova ngwa moyo; ndipo lidalitsike thanthwe langa; nakwezeke Mulungu wa chipulumutso changa.


Khalani chete, ndipo dziwani kuti Ine ndine Mulungu, Ndidzabuka mwa amitundu, ndidzabuka padziko lapansi.


Kwezekani m'mwambamwamba, Mulungu; ulemerero wanu ukhale pamwamba m'dziko lonse lapansi.


Mukwezeke m'mwambamwamba, Mulungu; ulemerero wanu ukhale pamwamba padziko lonse lapansi.


Ufumu wanu udze. Kufuna kwanu kuchitidwe, monga Kumwamba chomwecho pansi pano.


Ndipo musatitengere kokatiyesa, koma mutipulumutse kwa woipayo.


nati, Tikuyamikani, Ambuye Mulungu, Wamphamvuyonse, amene muli, nimunali; popeza mwadzitengera mphamvu yanu yaikulu, ndipo mwachita ufumu.


Kondwera pa iye, m'mwamba iwe, ndi oyera mtima, ndi atumwi, ndi aneneri inu; chifukwa Mulungu anauweruzira kuweruzidwa kwanu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa