Masalimo 21:11 - Buku Lopatulika11 Pakuti anakupangirani choipa, anapangana chiwembu, osakhoza kuchichita. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Pakuti anakupangirani choipa, anapangana chiwembu, osakhoza kuchichita. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Akafuna kuti aichite choipa ndi kuipweteka, adzalephereratu, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Ngakhale iwo akukonzereni chiwembu mwa kuchenjera kwawo sadzapambana; Onani mutuwo |