Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 21:10 - Buku Lopatulika

10 Mudzaziononga zobala zao kuzichotsa padziko lapansi, ndi mbeu zao mwa ana a anthu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Mudzaziononga zobala zao kuzichotsa pa dziko lapansi, ndi mbeu zao mwa ana a anthu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Mfumuyo idzaononga ana ao pa dziko lapansi, zidzukulu zao zidzatha pakati pa anthu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Inu mudzawononga ana awo pa dziko lapansi, zidzukulu zawo pakati pa anthu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 21:10
8 Mawu Ofanana  

koma wakukhudza iyo adzikonzeratu chitsulo ndi luti la mkondo; ndipo idzatenthedwa konse ndi moto m'malo mwao.


Ndimo umu munali tchimo la nyumba ya Yerobowamu, limene linaidula ndi kuiononga padziko lapansi.


Phindu la m'nyumba mwake lidzachoka, akatundu ake adzamthawa tsiku la mkwiyo wake.


Zidzukulu zake zidulidwe; dzina lao lifafanizidwe mu mbadwo ukudza.


Pakuti Yehova akonda chiweruzo, ndipo sataya okondedwa ake. Asungika kosatha, koma adzadula mbumba za oipa.


Iwe sudzaphatikizidwa pamodzi nao poikidwa, pakuti iwe waononga dziko lako, wapha anthu ako; mbeu ya ochita zoipa sidzatchulidwa konse.


Pakuti taonani, likudza tsiku, lotentha ngati ng'anjo; ndipo onse akudzikuza ndi onse akuchita choipa. Adzakhala ngati chiputu; ndi tsiku lilinkudza lidzawayatsa, ati Yehova wa makamu, osawasiyira muzu kapena nthambi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa