Masalimo 2:11 - Buku Lopatulika11 Tumikirani Yehova ndi mantha, ndipo kondwerani ndi chinthenthe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Tumikirani Yehova ndi mantha, ndipo kondwerani ndi chinthenthe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tumikirani Chauta mwamantha ndi monjenjemera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Tumikirani Yehova mwa mantha ndi kukondwerera ulamuliro wake monjenjemera. Onani mutuwo |