Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 2:1 - Buku Lopatulika

1 Aphokoseranji amitundu, nalingiriranji anthu zopanda pake?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Aphokoseranji amitundu, nalingiriranji anthu zopanda pake?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Bwanji anthu akunja akufuna kuchita chiwembu? Chifukwa chiyani anthu ameneŵa akulingalira zopandapake?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Nʼchifukwa chiyani anthu a mitundu ina akufuna kuchita chiwembu? Akonzekeranji zopanda pake anthu?

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 2:1
21 Mawu Ofanana  

Pamenepo ndinawapera ngati fumbi la kumphepo; ndinawakhuthula ngati matope a pabwalo.


Pakuti anakupangirani choipa, anapangana chiwembu, osakhoza kuchichita.


Amitundu anapokosera, maufumu anagwedezeka, ananena mau, dziko lapansi linasungunuka.


Yehova wa makamu ali ndi ife; Mulungu wa Yakobo ndiye pamsanje pathu.


Ndidzakuyamikirani mwa anthu, Ambuye, ndidzakuimbirani mwa mitundu.


Musaiwale mau a iwo otsutsana ndi Inu; kusokosera kwa iwo akuukirani Inu kumakwera kosaleka.


Apangana mochenjerera pa anthu anu, nakhalira upo pa obisika anu.


Chitani phokoso, anthu inu, koma mudzathyokathyoka; tcherani khutu, inu nonse a maiko akutali; kwindani nokha, koma mudzathyokathyoka; kwindani nokha, koma mudzathyokathyoka.


Koma olimawo m'mene anaona mwanayo, ananena wina ndi mnzake, Uyo ndiye wolowa; tiyeni, timuphe, ndipo ife tidzatenga cholowa chake.


Pakuti adzampereka kwa amitundu, nadzamseka, nadzamchitira chipongwe, nadzamthira malovu;


Ndipo anakondwera, napangana naye kumpatsa ndalama.


Ndipo linagumukira iwo khamulo; ndipo oweruza anawang'ambira malaya ao; nalamulira kuti awakwapule.


Koma m'mene anamva iwo analaswa mtima, nafuna kuwapha.


Iwo adzachita nkhondo pa Mwanawankhosa, ndipo Mwanawankhosa adzawagonjetsa, chifukwa ali Mbuye wa ambuye, ndi Mfumu ya mafumu; ndipo adzawalakanso iwo akukhala naye, oitanidwa, ndi osankhika ndi okhulupirika.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa