Masalimo 16:9 - Buku Lopatulika9 Chifukwa chake wasekera mtima wanga, nukondwera ulemu wanga; mnofu wanganso udzakhala mokhazikika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Chifukwa chake wasekera mtima wanga, nukondwera ulemu wanga; mnofu wanganso udzakhala mokhazikika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Nchifukwa chake mtima wanga ukukondwa, ndipo m'katikati mwangamu ndikusangalala. Thupi langanso lidzakhala pabwino, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Choncho mtima wanga ndi wosangalala ndipo pakamwa panga pakukondwera; thupi langanso lidzakhala pabwino, Onani mutuwo |