Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 16:8 - Buku Lopatulika

8 Ndaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse; popeza ali padzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse; popeza ali pa dzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Nthaŵi zonse ndimalingalira za Chauta. Popeza kuti ali ku dzanja langa lamanja, palibe amene angandiopse konse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Ndayika Yehova patsogolo panga nthawi zonse. Popeza Iyeyo ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 16:8
13 Mawu Ofanana  

Popeza adzaima padzanja lamanja la waumphawi, kumpulumutsa kwa iwo akuweruza koipa moyo wake.


Ambuye padzanja lamanja lako adzaphwanya mafumu tsiku la mkwiyo wake.


Yehova ndiye wakukusunga; Yehova ndiye mthunzi wako wa kudzanja lako lamanja.


Ndikaziwerenga zichuluka koposa mchenga: Ndikauka ndikhalanso nanu.


Ndalama zake sakongoletsa mofuna phindu lalikulu, ndipo salandira chokometsera mlandu kutsutsa wosachimwa. Munthu wakuchita izi sadzagwedezeka kunthawi zonse.


Dzanja lanu lidzapeza adani anu onse, dzanja lanu lamanja lidzapeza iwo akuda Inu.


Mudzamvumvulukira munthu mpaka liti, kumupha iye, nonsenu, monga khoma lopendekeka, ndi mpanda woweyeseka?


Iye yekhayo ndiye thanthwe langa ndi chipulumutso changa, msanje wanga, sindidzagwedezeka.


Pa Mulungu pali chipulumutso changa ndi ulemerero wanga. Thanthwe la mphamvu yanga ndi pothawirapo panga mpa Mulungu.


Koma ndikhala ndi Inu chikhalire, mwandigwira dzanja langa la manja.


Likatha thupi langa ndi mtima wanga, Mulungu ndiye thanthwe la mtima wanga, ndi cholandira changa chosatha.


Ndi chikhulupiriro anasiya Ejipito, wosaopa mkwiyo wa mfumu; pakuti anapirira molimbika, monga ngati kuona wosaonekayo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa