Masalimo 16:5 - Buku Lopatulika5 Yehova ndiye gawo la cholowa changa ndi chikho changa, ndinu wondigwirira cholandira changa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Yehova ndiye gawo la cholowa changa ndi chikho changa, ndinu wondigwirira cholandira changa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Chauta ndiye chuma changa ndi choloŵa changa. Tsogolo langa lili m'manja mwanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Yehova, Inu mwandipatsa cholowa changa ndi chikho changa; mwateteza kolimba gawo langa. Onani mutuwo |