Masalimo 16:3 - Buku Lopatulika3 Za oyera mtima okhala padziko lapansi, iwo ndiwo omveka mbiri, mwa iwowo muli chikondwero changa chonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Za oyera mtima okhala pa dziko lapansi, iwo ndiwo omveka mbiri, mwa iwowo muli chikondwero changa chonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Kunena za oyera mtima amene ali pansi pano, ameneŵa ndi olemekezeka, ndipo ndimakondwera nawo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Kunena za oyera mtima amene ali pa dziko, amenewa ndi olemekezeka, amene ndimakondwera nawo. Onani mutuwo |