Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 150:2 - Buku Lopatulika

2 Mlemekezeni chifukwa cha ntchito zake zolimba; mlemekezeni monga mwa ukulu wake waunjinji.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Mlemekezeni chifukwa cha ntchito zake zolimba; mlemekezeni monga mwa ukulu wake waunjinji.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Mtamandeni chifukwa cha ntchito zake zamphamvu, mtamandeni chifukwa cha ukulu wake wopambana.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Mutamandeni chifukwa cha machitidwe ake amphamvu; mutamandeni chifukwa cha ukulu wake wopambana.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 150:2
8 Mawu Ofanana  

Kudziwitsa ana a anthu zamphamvu zake, ndi ulemerero waukulu wa ufumu wake.


Yehova ndi wamkulu, nayenera kulemekezedwa kwakukulu; ndi ukulu wake ngwosasanthulika.


Fotokozerani ulemerero wake mwa amitundu; zodabwitsa zake mwa mitundu yonse ya anthu.


Pakuti Yehova ndi wamkulu, nayenera kulemekezedwa kwakukulu; ayenera amuope koposa milungu yonse.


Ambuye Yehova, mwayamba Inu kuonetsera mtumiki wanu ukulu wanu, ndi dzanja lanu lamphamvu; pakuti Mulungu ndani m'mwamba kapena padziko lapansi wakuchita monga mwa ntchito zanu, ndi monga mwa mphamvu zanu?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa