Masalimo 149:9 - Buku Lopatulika9 kuwachitira chiweruzo cholembedwacho. Ulemu wa okondedwa ake onse ndi uwu. Aleluya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 kuwachitira chiweruzo cholembedwacho. Ulemu wa okondedwa ake onse ndi uwu. Aleluya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 kuti aŵalange monga momwe Mulungu adalamulira. Umenewu ndiwo ulemerero wa anthu okhulupirira Chauta. Tamandani Chauta! Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 kuchita zimene zinalembedwa zotsutsana nawo Uwu ndi ulemerero wa oyera mtima ake onse. Tamandani Yehova. Onani mutuwo |