Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 149:8 - Buku Lopatulika

8 kumanga mafumu ao ndi maunyolo, ndi omveka ao ndi majerejede achitsulo,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 kumanga mafumu ao ndi maunyolo, ndi omveka ao ndi majerejede achitsulo,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Amange mafumu ao ndi maunyolo, amange atsogoleri ao ndi zitsulo,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 kumanga mafumu awo ndi zingwe, anthu awo otchuka ndi unyolo wachitsulo,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 149:8
4 Mawu Ofanana  

Ndipo akamangidwa m'nsinga, nakakodwa ndi zingwe za mazunzo,


Ndipo awa ndi mafumu a dzikolo amene Yoswa ndi ana a Israele anawakantha tsidya lija la Yordani kumadzulo, kuyambira Baala-Gadi m'chigwa cha Lebanoni mpaka phiri la Halaki lokwera kunka ku Seiri; ndipo Yoswa analipereka kwa mafuko a Israele, likhale laolao, monga mwa magawo ao;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa