Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 147:9 - Buku Lopatulika

9 Amene apatsa zoweta chakudya chao, ana a khwangwala alikulira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Amene apatsa zoweta chakudya chao, ana a khungubwi alikulira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Amapereka chakudya kwa nyama ndi kwa ana a khungubwi pamene akulira chakudya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Iye amapereka chakudya kwa ngʼombe ndi kwa ana a makwangwala pamene akulira chakudya.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 147:9
7 Mawu Ofanana  

Ndipo iwe udzitengereko wekha zakudya zonse zodyedwa, nudzisonkhanitsire izi wekha: ndipo zidzakhala zakudya za iwe ndi za iwo.


Amkonzeratu khwangwala chakudya chake ndani, pamenepo ana ake afuulira kwa Mulungu, naulukauluka osowa chakudya?


Ndiye wakupatsa nyama zonse chakudya; pakuti chifundo chake nchosatha.


Yang'anirani mbalame za kumwamba, kuti sizimafesa ai, kapena sizimatema ai, kapena sizimatutira m'nkhokwe; ndipo Atate wanu wa Kumwamba azidyetsa. Nanga inu mulibe kusiyana nazo kuziposa kodi?


Lingirirani makwangwala, kuti samafesai, kapena kutemai; alibe nyumba yosungiramo, kapena nkhokwe; ndipo Mulungu awadyetsa; nanga inu simuziposa mbalame kwambiri!


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa