Masalimo 147:8 - Buku Lopatulika8 Amene aphimba thambo ndi mitambo, amene akonzera mvula nthaka, amene aphukitsa msipu pamapiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Amene aphimba thambo ndi mitambo, amene akonzera mvula nthaka, amene aphukitsa msipu pamapiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Amaphimba zakumwamba ndi mitambo, amapatsa nthaka mvula, amameretsa udzu pa magomo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Iye amaphimba mlengalenga ndi mitambo; amapereka mvula ku dziko lapansi ndi kumeretsa udzu mʼmapiri. Onani mutuwo |