Masalimo 147:7 - Buku Lopatulika7 Yamikani Yehova ndi kuthira mang'ombe; muimbireni Mulungu wathu zomlemekeza pazeze: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Yamikani Yehova ndi kuthira mang'ombe; muimbireni Mulungu wathu zomlemekeza pazeze: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Imbirani Chauta mothokoza, imbirani Mulungu wathu nyimbo yokoma ndi pangwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Imbirani Yehova ndi mayamiko; imbani nyimbo kwa Mulungu ndi pangwe. Onani mutuwo |