Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 147:4 - Buku Lopatulika

4 Awerenga nyenyezi momwe zili; azitcha maina zonsezi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Awerenga nyenyezi momwe zili; azitcha maina zonsezi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Amadziŵa chiŵerengero cha nyenyezi, zonse amazitcha maina ake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Amadziwa chiwerengero cha nyenyezi, ndipo iliyonse amayitchula dzina.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 147:4
4 Mawu Ofanana  

Ndipo anamtulutsa iye kunja, nati, Tayang'anatu kumwamba, uwerenge nyenyezi, ngati ukhoza kuziwerenga zimenezo: ndipo anati kwa iye, Zoterezo zidzakhala mbeu zako.


Mlemekezeni, dzuwa ndi mwezi; mlemekezeni, nyenyezi zonse zounikira.


Pakuona ine thambo la kumwamba lanu, ntchito ya zala zanu, mwezi ndi nyenyezi, zimene munazikhazika,


Kwezani maso anu kumwamba, muone amene analenga izo, amene atulutsa khamu lao ndi kuziwerenga; azitcha zonse maina ao, ndi mphamvu zake zazikulu, ndi popeza ali wolimba mphamvu, palibe imodzi isoweka.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa