Masalimo 143:6 - Buku Lopatulika6 Nditambalitsira manja anga kwa Inu: Moyo wanga ulira Inu monga dziko lolira mvula. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Nditambalitsira manja anga kwa Inu: Moyo wanga ulira Inu monga dziko lolira mvula. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Ndimatambalitsira manja anga kwa Inu, mtima wanga umamva ludzu lofuna Inu, monga limachitira dziko louma. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Ndatambalitsa manja anga kwa Inu; moyo wanga uli ndi ludzu lofuna Inu monga nthaka yowuma. Sela Onani mutuwo |