Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 143:5 - Buku Lopatulika

5 Ndikumbukira masiku a kale lomwe; zija mudazichita ndilingirirapo; ndikamba pandekha za ntchito ya manja anu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndikumbukira masiku a kale lomwe; zija mudazichita ndilingirirapo; ndikamba pandekha za ntchito ya manja anu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Ndimakumbukira masiku amakedzana, ndimasinkhasinkha za zonse zimene mwazichita, ndimalingalira ntchito za manja anu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Ndimakumbukira masiku amakedzana; ndimalingalira za ntchito yanu yonse, ndimaganizira zimene manja anu anachita.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 143:5
10 Mawu Ofanana  

Ndipo Isaki anatuluka kulingalira m'munda madzulo; ndipo anatukula maso ake, nayang'ana, taona, ngamira zinalinkudza.


Anachita chokumbukitsa zodabwitsa zake; Yehova ndiye wachisomo ndi nsoni zokoma.


Mulungu wanga, moyo wanga udziweramira m'kati mwanga; chifukwa chake ndikumbukira Inu m'dziko la Yordani, ndi mu Aheremoni, m'kaphiri ka Mizara.


Anthu anga, kumbukiranitu chofunsira Balaki mfumu ya Mowabu, ndi chomuyankha Balamu mwana wa Beori, kuyambira ku Sitimu kufikira ku Giligala; kuti mudziwe zolungama za Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa