Masalimo 143:4 - Buku Lopatulika4 Potero mzimu wanga wakomoka mwa ine; mtima wanga utenga nkhawa m'kati mwanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Potero mzimu wanga wakomoka mwa ine; mtima wanga utenga nkhawa m'kati mwanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Nchifukwa chake mtima wanga wafooka m'kati mwanga, mumtima mwangamu mukuchita mantha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Choncho mzimu wanga ukufowoka mʼkati mwanga; mʼkati mwanga, mtima wanga uli ndi nkhawa. Onani mutuwo |