Masalimo 143:3 - Buku Lopatulika3 Pakuti mdani alondola moyo wanga; apondereza pansi moyo wanga; andikhalitsa mumdima monga iwo adafa kale lomwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pakuti mdani alondola moyo wanga; apondereza pansi moyo wanga; andikhalitsa mumdima monga iwo adafa kale lomwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mdani wandilondola, wavimviniza moyo wanga m'dothi, wandikhazika mu mdima, ngati anthu amene adafa kale. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Mdani akundithamangitsa, iye wandipondereza pansi; wachititsa kuti ndikhale mu mdima ngati munthu amene anafa kale. Onani mutuwo |