Masalimo 143:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo musaitane mlandu wa mtumiki wanu; pakuti pamaso panu sipadzakhala wolungama wamoyo mmodzi yense. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo musaitane mlandu wa mtumiki wanu; pakuti pamaso panu sipadzakhala wolungama wamoyo mmodzi yense. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Musandizenge mlandu ine mtumiki wanu, popeza kuti palibe munthu wamoyo amene ali wolungama pamaso panu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Musazenge mlandu mtumiki wanu, pakuti palibe munthu wamoyo amene ndi wolungama pamaso panu. Onani mutuwo |
koma podziwa kuti munthu sayesedwa wolungama pa ntchito ya lamulo, koma mwa chikhulupiriro cha Yesu Khristu, ifedi tinakhulupirira kwa Khristu Yesu, kuti tikayesedwe olungama ndi chikhulupiriro cha Khristu, ndipo si ndi ntchito za lamulo; pakuti palibe munthu adzayesedwa wolungama ndi ntchito za lamulo.