Masalimo 143:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo mwa chifundo chanu mundidulire adani anga, ndipo muononge onse akusautsa moyo wanga; pakuti ine ndine mtumiki wanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo mwa chifundo chanu mundidulire adani anga, ndipo muononge onse akusautsa moyo wanga; pakuti ine ndine mtumiki wanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Kanthani adani anga chifukwa cha chikondi chanu chosasinthika pa ine. Muwononge onse ondizunza, pakuti ine ndine mtumiki wanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Mwa chikondi chanu chosasinthika khalitsani chete adani anga; wonongani adani anga, pakuti ndine mtumiki wanu. Onani mutuwo |