Masalimo 144:1 - Buku Lopatulika1 Wolemekezeka Yehova thanthwe langa, wakuphunzitsa manja anga achite nkhondo, zala zanga zigwirane nao: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Wolemekezeka Yehova thanthwe langa, wakuphunzitsa manja anga achite nkhondo, zala zanga zigwirane nao: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Atamandike Chauta, thanthwe langa londitchinjiriza, amene amaphunzitsa manja anga ndi zala zanga kumenya nkhondo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Atamandike Yehova Thanthwe langa, amene amaphunzitsa manja anga kuchita nkhondo; zala zanga kumenya nkhondo. Onani mutuwo |