Masalimo 141:9 - Buku Lopatulika9 Mundisunge ndisagwe mumsampha ananditcherawo, ndisakodwe m'makwekwe a iwo ochita zopanda pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Mundisunge ndisagwe mumsampha ananditcherawo, ndisakodwe m'makwekwe a iwo ochita zopanda pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Mundipulumutse ku msampha umene iwo anditchera, ndi ku makhwekhwe a anthu ochita zoipa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Mundipulumutse ku misampha imene anditchera, ku makhwekhwe amene anthu oyipa andikonzera. Onani mutuwo |