Masalimo 141:8 - Buku Lopatulika8 Pakuti maso anga apenya kwanu, Yehova Ambuye; ndithawira kwa Inu; musataye moyo wanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Pakuti maso anga apenya kwanu, Yehova Ambuye; ndithawira kwa Inu; musataye moyo wanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Koma maso anga amayang'anirabe kwa Inu, Chauta Mulungu wanga. Ndimathaŵira kwa Inu kuti munditeteze, musandisiye opanda wonditchinjiriza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Koma maso anga akupenyetsetsa Inu Ambuye Wamphamvuzonse; ndimathawira kwa Inu, musandipereke ku imfa. Onani mutuwo |