Masalimo 141:7 - Buku Lopatulika7 Mafupa athu amwazika pakamwa pa manda, monga ngati akumba nanyimphula nthaka yapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Mafupa athu amwazika pakamwa pa manda, monga ngati akumba nanyimphula nthaka yapansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Monga momwe nkhuni zimamwazikira akaziŵaza, ndi m'menenso mafupa ao adzamwazikira ku manda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Iwo adzati, “Monga momwe nkhuni zimamwazikira akaziwaza, ndi momwenso mafupa athu amwazikira pa khomo la manda.” Onani mutuwo |