Masalimo 141:6 - Buku Lopatulika6 Oweruza ao anagwetseka pambali pa thanthwe; nadzamva mau anga kuti ndiwo okondweretsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Oweruza ao anagwetseka pambali pa thanthwe; nadzamva mau anga kuti ndiwo okondweretsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Anthu oipa akadzaperekedwa kwa oŵalanga, pamenepo adzaphunzira kuti mau a Chauta ndi oona. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Olamulira awo adzaponyedwa pansi kuchokera pa malo okwera kwambiri, ndipo anthu oyipa adzaphunzira kuti mawu anga anayankhulidwa bwino. Onani mutuwo |