Masalimo 141:10 - Buku Lopatulika10 Oipa agwe pamodzi m'maukonde ao, kufikira nditapitirira ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Oipa agwe pamodzi m'maukonde ao, kufikira nditapitirira ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Anthu oipa akodwe pamodzi mu ukonde wao womwe, koma ine ndipulumuke. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Anthu oyipa akodwe mʼmaukonde awo, mpaka ine nditadutsa mwamtendere. Onani mutuwo |