Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 142:1 - Buku Lopatulika

1 Ndifuula nalo liu langa kwa Yehova; ndi mau anga ndipemba kwa Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Ndifuula nalo liu langa kwa Yehova; ndi mau anga ndipemba kwa Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Ndikulirira Chauta mokweza, ndikupemba kwa Chauta mofuula.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Ndikulirira Yehova mofuwula; ndikukweza mawu anga kwa Yehova kupempha chifundo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 142:1
12 Mawu Ofanana  

Ndipo Yabezi anaitana kwa Mulungu wa Israele, ndi kuti, Mundidalitse ndithu, ndi kukulitsa malire anga; ndi dzanja lanu likhale ndi ine, nimundisunge, kuti choipa chisandivute. Ndipo Mulungu anafikitsa chopempha iye.


Yehova, ndaitana kwa Inu; ndifulumireni ine; munditcherere khutu, pamene ndiitana kwa Inu.


Mverani mau a kupemba kwanga, pamene ndilirira Inu, pamene ndikweza manja anga kuloza ponenera panu poyera.


Ndinafuulira kwa Inu, Yehova; kwa Ambuye ndinapemba,


Wodala munthuyo wokhululukidwa tchimo lake; wokwiriridwa choipa chake.


Ndipulumutseni, Mulungu, mwa dzina lanu, ndipo mundiweruze ndi mphamvu yanu.


Mundichitire chifundo, Mulungu, mundichitire chifundo; pakuti moyo wanga ukhulupirira Inu, ndipo ndithawira kumthunzi wa mapiko anu, kufikira zosakazazo zidzapita.


(amenewo dziko lapansi silinayenere iwo), osokerera m'mapululu, ndi m'mapiri, ndi m'mapanga, ndi m'mauna a dziko.


Ndipo panjira anafika ku makola a nkhosa, kumene kunali phanga; ndipo Saulo analowa kuti akadzithandize. Ndipo Davide ndi anyamata ake analikukhala m'kati mwa phangamo.


Ndipo anyamata a Davide ananena naye, Onani, lero ndilo tsiku limene Yehova anati kwa inu, Onani, Ine ndidzapereka mdani wako m'dzanja lako, kuti ukamchitira iye chokukomera. Ndipo Davide ananyamuka, nadula mkawo wa mwinjiro wa Saulo mobisika.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa