Masalimo 141:3 - Buku Lopatulika3 Muike mdindo pakamwa panga, Yehova; sungani pakhomo pa milomo yanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Muike mdindo pakamwa panga, Yehova; sungani pakhomo pa milomo yanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Muike mlonda pakamwa panga, Inu Chauta. Mulonde pa khomo la milomo yanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Yehova ikani mlonda pakamwa panga; londerani khomo la pa milomo yanga. Onani mutuwo |