Masalimo 140:8 - Buku Lopatulika8 Yehova, musampatse woipa zokhumba iye; musamthandize zodzipanga zake; angadzikuze. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Yehova, musampatse woipa zokhumba iye; musamthandize zodzipanga zake; angadzikuze. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Inu Chauta, musampatse munthu woipa zokhumba zake. Musathandizire chiwembu chake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Musawapatse anthu oyipa zokhumba zawo, Inu Yehova; musalole kuti zokonza zawo zitheke, mwina iwo adzayamba kunyada. Sela Onani mutuwo |