Masalimo 140:9 - Buku Lopatulika9 Kunena za mutu wao wa iwo akundizinga, choipa cha milomo yao chiwaphimbe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Kunena za mutu wao wa iwo akundizinga, choipa cha milomo yao chiwaphimbe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Adani anga ondizinga asandigonjetse. Mau ao otemberera aŵabwerere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Mitu ya amene andizungulira iphimbidwe ndi masautso amene milomo yawo yayambitsa. Onani mutuwo |