Masalimo 140:5 - Buku Lopatulika5 Odzikuza ananditchera msampha, nandibisira zingwe; anatcha ukonde m'mphepete mwa njira; ananditchera makwekwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Odzikuza ananditchera msampha, nandibisira zingwe; anatcha ukonde m'mphepete mwa njira; ananditchera makwekwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Anthu odzikuza anditchera msampha mobisika, atchera ukonde wa zingwe, anditchera misampha m'mbali mwa njira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Anthu odzikuza anditchera msampha mobisika; iwo atchera zingwe za maukonde awo ndipo anditchera misampha pa njira yanga. Sela Onani mutuwo |