Masalimo 140:4 - Buku Lopatulika4 Ndilindireni Yehova, ndisalowe m'manja mwa woipa; ndisungeni kwa munthu wachiwawa; kwa iwo akuti akankhe mapazi anga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndilindireni Yehova, ndisalowe m'manja mwa woipa; ndisungeni kwa munthu wachiwawa; kwa iwo akuti akankhe mapazi anga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Inu Chauta, tetezeni kwa anthu oipa, tchinjirizeni kwa anthu andeu, amene amaganiza zofuna kundigwetsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Tetezeni Inu Yehova, kwa anthu oyipa; tchinjirizeni kwa anthu ankhanza amene amakonza zokola mapazi anga. Onani mutuwo |